Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+ Miyambo 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wochita ubwenzi ndi mbala akudana ndi moyo wake.+ Iye angamve lumbiro lokhudza temberero, koma osakanena chilichonse.+ 1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+
24 Wochita ubwenzi ndi mbala akudana ndi moyo wake.+ Iye angamve lumbiro lokhudza temberero, koma osakanena chilichonse.+
16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+