Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano popeza kuti ife talumbira+ pali Yehova kuti sitiwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo,+ tichita chiyani ndi anthu amene atsala opanda akaziwa?”

  • 1 Samueli 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Motero amuna a Isiraeli anatopa kwambiri pa tsiku limenelo, komabe Sauli analumbirira+ anthuwo kuti: “Munthu aliyense wodya mkate dzuwa lisanalowe, komanso ndisanabwezere+ adani anga, ndi wotembereredwa!” Choncho panalibe aliyense mwa anthuwo amene anadya mkate.+

  • Mateyu 5:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+

  • Maliko 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndithu, anachita kumulumbirira kuti: “Chilichonse chimene ungapemphe kwa ine, ndidzachipereka kwa iwe,+ ngakhale hafu ya ufumu wangawu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena