Numeri 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli. Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Deuteronomo 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+ Salimo 136:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anapha Sihoni mfumu ya Aamori:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
23 Koma Sihoni sanalole kuti Aisiraeli adzere m’dziko lake.+ M’malomwake, iye anasonkhanitsa anthu ake onse n’kupita kukamenyana ndi Aisiraeli m’chipululumo. Anakafika ku Yahazi,+ kumene anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
31 “Zitatero, Yehova anandiuza kuti, ‘Taona, ndikupereka Sihoni ndi dziko lake kwa iwe. Yamba kulanda dziko lake.’+
19 Iye anapha Sihoni mfumu ya Aamori:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+