Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno chifukwa choti wachimwira malo oyera azilipira mwa kubweza zinthu zopatulikazo ndiponso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu+ a malipirowo. Malipirowo aziwapereka kwa wansembe, ndipo mwa kupereka nkhosa ya nsembe ya kupalamula, wansembeyo aziphimba machimo+ a munthuyo ndipo azikhululukidwa.+

  • Levitiko 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo azikhululukidwa chilichonse mwa zonse zimene angachite zom’palamulitsa.”

  • Levitiko 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Nsembe ya kupalamula ndi yofanana ndi nsembe yamachimo. Zonsezi lamulo lake ndi limodzi.+ Nyama ya nsembe yophimba machimo izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena