Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsa ndithu+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti likhale cholowa chako.+

  • Deuteronomo 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ukaiwala mtolo wa tirigu pokolola m’munda wako,+ usabwerere kukatenga mtolowo. Uzisiyira mlendo wokhala m’dziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+ Uzichita zimenezi kuti Yehova Mulungu wako akudalitse pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita.+

  • Salimo 41:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Wodala ndi munthu amene amachita zinthu moganizira munthu wonyozeka.+

      Pa tsiku la tsoka, Yehova adzamupulumutsa.+

  • Miyambo 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Wa diso labwino adzadalitsidwa, chifukwa amapereka chakudya chake kwa munthu wonyozeka.+

  • Yesaya 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma munthu wopatsa amapereka malangizo okhudza kupatsa, ndipo iyeyo amapitiriza kukhala wopatsa.+

  • 2 Akorinto 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso, Mulungu akhoza kuchititsa kuti kukoma mtima kwake konse kwakukulu kusefukire kwa inu. Choncho nthawi zonse mudzakhala ndi zinthu zokwanira kusamalira zosowa zanu, ndipo mudzakhalanso ndi zinthu zambiri zogwiritsa ntchito pa ntchito iliyonse yabwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena