Numeri 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zofunkhazo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa khamu la anthuwo.+ 1 Samueli 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndani angamve zimene mukunenazo? Pakuti gawo limene munthu amene anapita kunkhondo alandire, likhala lofanana ndi gawo limene munthu amene anali kulondera katundu alandire.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+ Salimo 68:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+
27 Zofunkhazo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa khamu la anthuwo.+
24 Ndani angamve zimene mukunenazo? Pakuti gawo limene munthu amene anapita kunkhondo alandire, likhala lofanana ndi gawo limene munthu amene anali kulondera katundu alandire.+ Aliyense alandirapo kenakake.”+
12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+