Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Zofunkhazo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa khamu la anthuwo.+

  • Yoswa 22:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anawauza kuti: “Bwererani kumahema anu ndi chuma chambiri ndiponso ziweto zambiri, ndi siliva, golide, mkuwa, zitsulo, ndi zovala zambiri.+ Tengani katundu amene munafunkha+ kwa adani anu n’kugawana ndi abale anu.”

  • Salimo 68:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+

      Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+

  • 1 Timoteyo 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena