Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+

  • Deuteronomo 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+

  • Oweruza 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kodi aliyense amene mulungu wako Kemosi+ wakuchititsa kuti umugonjetse, si amene udzam’gonjetsa? Chotero aliyense amene Yehova Mulungu wathu wam’gonjetsa pamaso pathu ndi amenenso ife tidzam’gonjetsa.+

  • Nehemiya 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho ana awo+ analowa ndi kutenga dzikolo,+ ndipo munagonjetsa+ anthu okhala m’dzikolo, Akanani,+ ndi kuwapereka m’manja mwawo. Munaperekanso ngakhale mafumu a Akananiwo+ ndi mitundu ya anthu ya m’dzikolo+ kwa ana a Isiraeliwo kuti awachite zimene akufuna.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena