Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ Deuteronomo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Popitiriza, iye anapereka dalitso lotsatirali kwa Yuda,+ kuti:“Inu Yehova, imvani mawu a Yuda,+M’bweretseni kwa anthu ake.Manja ake amenya nkhondo pofuna kulanditsa zinthu zake.Mukhaletu mthandizi wake kwa adani ake.”+
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+
7 Popitiriza, iye anapereka dalitso lotsatirali kwa Yuda,+ kuti:“Inu Yehova, imvani mawu a Yuda,+M’bweretseni kwa anthu ake.Manja ake amenya nkhondo pofuna kulanditsa zinthu zake.Mukhaletu mthandizi wake kwa adani ake.”+