Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+

  • Oweruza 21:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pamapeto pake anati: “Pajatu ku Silo+ kumachitika chikondwerero cha Yehova chaka ndi chaka. Mzinda wa Silo uli kum’mwera kwa Beteli, chakum’mawa kwa msewu waukulu wochokera ku Beteli kupita ku Sekemu,+ ndiponso chakum’mwera kwa Lebona.”

  • 1 Samueli 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chaka ndi chaka mwamuna ameneyu anali kutuluka mumzinda wake n’kupita ku Silo,+ kukagwada ndi kuweramira pansi+ pamaso pa Yehova wa makamu ndi kupereka nsembe zake. Kumeneko n’kumene ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ anali kutumikira monga ansembe a Yehova.+

  • Yeremiya 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena