Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ‘Pakati panu papezeka anthu opanda pake+ amene akufuna kupatutsa anthu mumzinda wawo,+ ponena kuti: “Tiyeni tikatumikire milungu ina,” milungu imene inu simunaidziwe,’

  • Oweruza 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyetu tipatseni amunawo,+ anthu opanda pakewo,+ amene ali mu Gibeya,+ kuti tiwaphe+ ndi kuchotsa choipachi mu Isiraeli.”+ Koma ana a Benjamini sanafune kumvera mawu a abale awo, ana a Isiraeli.+

  • Miyambo 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu wopanda pake,+ wochita zopweteka anzake, amayenda ndi mawu opotoka.+

  • Miyambo 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Munthu wopanda pake amafukula zinthu zoipa,+ ndipo pakamwa pake pamakhala mawu okhala ngati makala amoto.+

  • Nahumu 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Taonani mapazi a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino.+ Iye akulengeza za mtendere. Iwe Yuda, chita zikondwerero zako.+ Kwaniritsa zimene walonjeza+ chifukwa palibe munthu aliyense wopanda pake amene adzadutsa pakati pako.+ Munthu wopanda pakeyo adzaphedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena