Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo mneneri+ kapena wolota malotoyo muzimupha,+ chifukwa walankhula mopandukira Yehova Mulungu wanu amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo ndi kukuwombolani m’nyumba yaukapolo. Munthu ameneyo walankhula zimenezo kuti akupatutseni panjira imene Yehova Mulungu wanu anakulamulani kuyendamo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Deuteronomo 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Deuteronomo 22:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Mwamuna akapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake,+ mwamuna ndi mkaziyo, onsewo azifera pamodzi. Mwamuna wogona ndi mkaziyo ndiponso mkaziyo azifera pamodzi.+ Motero uzichotsa oipawo mu Isiraeli.+

  • 1 Akorinto 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chimene mukudzitamira+ si chabwino ayi. Kodi simukudziwa kuti chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa+ mtanda wonse?+

  • 1 Akorinto 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ndipo Mulungu amaweruza amene ali kunja?+ “M’chotseni pakati panu munthu woipayo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena