Oweruza 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nayenso mdzakazi* wake wa ku Sekemu, anamubalira mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lakuti Abimeleki.+ Oweruza 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti: Oweruza 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako nzika zonse za Sekemu ndi anthu onse m’nyumba ya Milo+ anasonkhana pamodzi kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu+ ku Sekemu.+ Kumeneko analonga Abimeleki ufumu.+
31 Nayenso mdzakazi* wake wa ku Sekemu, anamubalira mwana wamwamuna, ndipo anamutcha dzina lakuti Abimeleki.+
9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti:
6 Kenako nzika zonse za Sekemu ndi anthu onse m’nyumba ya Milo+ anasonkhana pamodzi kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu+ ku Sekemu.+ Kumeneko analonga Abimeleki ufumu.+