Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho anakhala pansi ndipo onse awiri anayamba kudya ndi kumwera pamodzi. Kenako bambo a mtsikanayo anauza mwamunayo kuti: “Chonde, lero mugone, mupite mawa,+ ndipo musangalatse mtima wanu.”+

  • Salimo 104:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+

      Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+

      Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+

  • Mlaliki 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa ndi kusangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+

  • Mlaliki 10:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chakudya chimachititsa antchito kuseka, ndipo vinyo amachititsa moyo kusangalala,+ koma ndalama zimathandiza pa zinthu zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena