Miyambo 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chinyengo chimakhala mumtima mwa anthu okonza chiwembu,+ koma olimbikitsa mtendere amasangalala.+ Miyambo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu okonza chiwembu amasochera,+ koma anthu okonzekera kuchita zabwino amapeza kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+ Miyambo 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye amatsinzinira ndi maso ake pokonza ziwembu.+ Amalumirira mano, ndipo amakwanitsadi kuchita chiwembu. Miyambo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Aliyense wokonzera anzake ziwembu adzatchedwa katswiri wa maganizo oipa.+
22 Anthu okonza chiwembu amasochera,+ koma anthu okonzekera kuchita zabwino amapeza kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+
30 Iye amatsinzinira ndi maso ake pokonza ziwembu.+ Amalumirira mano, ndipo amakwanitsadi kuchita chiwembu.