Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ Yoswa 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano, chonde lumbirani kwa ine pali Yehova,+ kuti chifukwa choti ndakusonyezani kukoma mtima kosatha, inunso mudzasonyeza anthu a m’nyumba ya bambo anga+ kukoma mtima kosatha, ndipo mundipatse chizindikiro chodalirika.+ Yoswa 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+
12 Tsopano, chonde lumbirani kwa ine pali Yehova,+ kuti chifukwa choti ndakusonyezani kukoma mtima kosatha, inunso mudzasonyeza anthu a m’nyumba ya bambo anga+ kukoma mtima kosatha, ndipo mundipatse chizindikiro chodalirika.+
15 Choncho Yoswa anagwirizana nawo za mtendere,+ ndipo anachita nawo pangano kuti asawaphe. Zitatero, atsogoleri+ a Isiraeli analumbira kwa anthuwo.+