Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 21:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Zitatero, Abulahamu anabzala mtengo wa bwemba pa Beere-seba, n’kuitanirapo dzina la Yehova,+ Mulungu wanthawi zonse.+

  • 1 Samueli 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Sauli anamva kuti Davide ndi anthu amene anali naye apezeka. Iye anamva zimenezi ali ku Gibeya pamalo okwezeka, atakhala pansi pa mtengo wa bwemba.+ Sauliyo anali atagwira mkondo+ m’manja mwake ndipo atumiki ake onse anali atamuzungulira.

  • 1 Mbiri 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero amuna onse olimba mtima ananyamuka n’kukanyamula mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake n’kupita nayo ku Yabesi. Atatero anakafotsera mafupa awo pansi pa mtengo waukulu+ ku Yabesiko.+ Kenako anasala kudya+ masiku 7.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena