Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anayamba kulonjeza+ kuti: “Inu Yehova wa makamu, mukaona nsautso yanga, ine kapolo wanu wamkazi,+ ndi kundikumbukira,+ ndiponso ngati simudzaiwala kapolo wanu wamkazi ndi kum’patsa mwana wamwamuna, ndidzam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake, ndipo lezala silidzadutsa m’mutu mwake.”+

  • 1 Samueli 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo Eli anamuyankha kuti: “Pita mu mtendere,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wam’pempha.”+

  • Salimo 66:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+

      Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+

  • Mateyu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.

  • 1 Yohane 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso, popeza timadziwa kuti amatimvera tikapempha chilichonse,+ timakhala ndi chikhulupiriro kuti tilandira zinthu zimene tamupemphazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena