1 Samueli 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi, dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali mikono 6 ndi chikhatho chimodzi.*+ 1 Mbiri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani+ mwana wa Yairi anapha Lami m’bale wake wa Goliyati+ Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+
4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi, dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali mikono 6 ndi chikhatho chimodzi.*+
5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani+ mwana wa Yairi anapha Lami m’bale wake wa Goliyati+ Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+