Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Taona, ukukhala pafupi ndi Simeyi+ wa ku Bahurimu,+ mwana wa Gera M’benjamini. Iyeyu ananditemberera temberero lopweteka+ tsiku limene ndinkapita ku Mahanaimu.+ Ndi iyeyu amene anabwera kudzakumana nane pa Yorodano,+ choncho ndinamulumbirira pamaso pa Yehova kuti: ‘Sindidzakupha ndi lupanga.’+

  • 1 Mafumu 2:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Zikadzachitika kuti tsiku lina wachoka n’kudutsa chigwa* cha Kidironi,+ udziwiretu kuti udzafa ndithu.+ Mlandu wa magazi ako udzakhala pamutu pako.”+

  • 1 Mafumu 2:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Itatero, mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada amene ananyamuka n’kukakantha Simeyi, ndipo anafa.+

      Choncho ufumuwo unakhazikika m’manja mwa Solomo.+

  • Aheberi 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena