Oweruza 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+ Oweruza 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno amuna a ku Efuraimu anasonkhana pamodzi n’kuwolokera tsidya lina chakumpoto, ndi kuuza Yefita kuti: “N’chifukwa chiyani unawoloka kukamenya ndi ana a Amoni ife osatiitana kuti tipite nawe?+ Tikutentha ndi moto pamodzi ndi nyumba yako.”+
8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+
12 Ndiyeno amuna a ku Efuraimu anasonkhana pamodzi n’kuwolokera tsidya lina chakumpoto, ndi kuuza Yefita kuti: “N’chifukwa chiyani unawoloka kukamenya ndi ana a Amoni ife osatiitana kuti tipite nawe?+ Tikutentha ndi moto pamodzi ndi nyumba yako.”+