Yoswa 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu a ku Gibeoni+ anamva zimene Yoswa anachita ku Yeriko+ ndi Ai.+ Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+ Yoswa 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+
27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.