Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+ Mlaliki 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene chinakhalapo chinapatsidwa kale dzina, ndipo zinadziwika kale kuti munthu ndi ndani.+ Iye sangathe kudziteteza pa mlandu wotsutsana ndi amene ali wamphamvu kuposa iyeyo.+
29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+
10 Chilichonse chimene chinakhalapo chinapatsidwa kale dzina, ndipo zinadziwika kale kuti munthu ndi ndani.+ Iye sangathe kudziteteza pa mlandu wotsutsana ndi amene ali wamphamvu kuposa iyeyo.+