Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 27:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Wotembereredwa ndi munthu wonyoza bambo ake kapena mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • Deuteronomo 27:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wavula bambo akewo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • 2 Samueli 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano lupanga+ silidzachoka panyumba yako mpaka kalekale.+ Chimenechi n’chotsatira cha zimene unachita chifukwa chondinyoza mwa kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala mkazi wako.’

  • Salimo 63:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Koma ofuna kuwononga moyo wanga,+

      Adzatsikira kumanda.+

  • Miyambo 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+

  • Miyambo 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Aliyense wotemberera bambo ake ndi mayi ake,+ nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+

  • Miyambo 30:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Diso limene limanyoza bambo ake ndiponso limene silimvera mayi ake,+ akhwangwala a kuchigwa* adzalikolowola ndipo ana a chiwombankhanga adzalidya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena