Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka n’kuthawa kutsatira Davide.

  • 1 Samueli 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde, bweretsa efodi+ kuno.” Pamenepo Abiyatara anapereka efodi kwa Davide.

  • 2 Samueli 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kumeneko kunalinso Zadoki+ pamodzi ndi Alevi+ onse atanyamula+ likasa+ la pangano la Mulungu woona. Choncho Aleviwo anatula pansi likasa la Mulungu woona pafupi ndi Abiyatara+ kufikira anthu onse atamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.

  • 1 Mbiri 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kuwonjezera pa amenewa, Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli,+ Asaya,+ Yoweli,+ Semaya,+ Elieli,+ ndi Aminadabu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena