2 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+ 1 Mafumu 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pomaliza mfumu inatuma anthu kukaitana Simeyi,+ ndipo inamuuza kuti: “Udzimangire nyumba ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usachoke kumeneko kupita kwina ndi kwina. 1 Mafumu 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+
5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+
36 Pomaliza mfumu inatuma anthu kukaitana Simeyi,+ ndipo inamuuza kuti: “Udzimangire nyumba ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usachoke kumeneko kupita kwina ndi kwina.
44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+