Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+ Ekisodo 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapanganso nyanga+ m’makona ake anayi. Nyanga zakezo zinatuluka m’makona akewo, ndipo guwalo analikuta ndi mkuwa.+ 1 Mafumu 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.
14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+
2 Anapanganso nyanga+ m’makona ake anayi. Nyanga zakezo zinatuluka m’makona akewo, ndipo guwalo analikuta ndi mkuwa.+
28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.