Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 16:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Komanso, ngati kuti kuyenda m’machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati inali nkhani yaing’ono,+ Ahabu anakwatira+ Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kukatumikira Baala+ ndi kum’gwadira.

  • 1 Mafumu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+

  • 1 Mafumu 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.”

  • 1 Mafumu 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.

  • 2 Mafumu 9:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Atatero, analowa m’nyumba ndipo anayamba kudya ndi kumwa, kenako anati: “Amuna inu, m’samaleni munthu wotembereredwayu.+ M’tengeni mukamuike m’manda, popeza ndi mwana wa mfumu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena