1 Mafumu 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova. 2 Mbiri 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ndikutumiza munthu waluso ndi wozindikira, dzina lake Hiramu-abi.+ 2 Mbiri 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira pake Hiramu anapanga ndowa,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Chotero iye anamaliza ntchito imene anali kugwirira Mfumu Solomo pa nyumba ya Mulungu woona.
40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova.
11 Pomalizira pake Hiramu anapanga ndowa,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Chotero iye anamaliza ntchito imene anali kugwirira Mfumu Solomo pa nyumba ya Mulungu woona.