1 Mafumu 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mfumu Solomo inatuma anthu kuti akatenge Hiramu+ ku Turo. 1 Mafumu 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova. 2 Mbiri 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira pake Hiramu anapanga ndowa,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Chotero iye anamaliza ntchito imene anali kugwirira Mfumu Solomo pa nyumba ya Mulungu woona. 2 Mbiri 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndowa, mafosholo,+ mafoloko,+ ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu-abivu+ anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova. Miyambo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi wamuona munthu waluso pa ntchito yake? Iye adzaima pamaso pa mafumu.+ Sadzaima pamaso pa anthu wamba.
40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova.
11 Pomalizira pake Hiramu anapanga ndowa,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Chotero iye anamaliza ntchito imene anali kugwirira Mfumu Solomo pa nyumba ya Mulungu woona.
16 ndowa, mafosholo,+ mafoloko,+ ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu-abivu+ anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.
29 Kodi wamuona munthu waluso pa ntchito yake? Iye adzaima pamaso pa mafumu.+ Sadzaima pamaso pa anthu wamba.