Ekisodo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+ 2 Mafumu 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira. 2 Mbiri 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndowa, mafosholo,+ mafoloko,+ ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu-abivu+ anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova. Yeremiya 52:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo,+ zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu ndi ziwiya zonse zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.+
3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+
14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.
16 ndowa, mafosholo,+ mafoloko,+ ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu-abivu+ anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.
18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo,+ zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu ndi ziwiya zonse zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.+