19 Pamasitepe 6 amenewo, panali zifaniziro 12 za mikango+ itaimirira, mbali iyi ndi iyi. Panalibenso ufumu wina umene unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.+
14 Ine ndidzakhala ngati mkango wamphamvu kwa Efuraimu+ ndiponso ngati mkango wamphongo kwa nyumba ya Yuda. Ineyo ndidzawakhadzulakhadzula ndekha ndi kuwataya ndipo sipadzakhala wowalanditsa.+