Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+ Deuteronomo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ndinatembenuka, n’kutsika m’phirimo,+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo m’likasa limene ndinapanga kuti izikhala mmenemo, monga mmene Yehova anandilamulira.+ Aheberi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.
13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+
5 Ndiyeno ndinatembenuka, n’kutsika m’phirimo,+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo m’likasa limene ndinapanga kuti izikhala mmenemo, monga mmene Yehova anandilamulira.+
4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.