Deuteronomo 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Limenelo ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso+ a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kuchiyambi kwa chaka mpaka kumapeto. 2 Mbiri 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano. 2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+
12 Limenelo ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso+ a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kuchiyambi kwa chaka mpaka kumapeto.
40 “Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone,+ ndipo makutu anu+ akhale tcheru kumvetsera pemphero lokhudza malo ano.
9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+