Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+

  • Deuteronomo 31:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pakuti ndikudziwa bwino kuti pambuyo pa imfa yanga, mosakayikira mudzachita zinthu zokuwonongetsani+ ndipo mudzapatuka ndi kusiya njira imene ndakulamulani kuyendamo. Pamapeto pake tsoka+ lidzakugwerani, chifukwa mudzachita zoipa pamaso pa Yehova ndi kumulakwira ndi ntchito za manja anu.”+

  • Oweruza 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anasiya Yehova ndi kuyamba kutumikira Baala ndi zifaniziro za Asitoreti.+

  • Salimo 106:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Anayamba kutumikira mafano awo,+

      Ndipo mafanowo anakhala msampha wawo.+

  • Ezekieli 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Kodi ndiwe wokonzeka kuwaweruza? Kodi uwaweruza, iwe mwana wa munthu?+ Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+

  • Machitidwe 7:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 inu amene munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachisunga.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena