-
2 Mafumu 9:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kenako Yehu anauza msilikali wake womuthandiza pagaleta+ dzina lake Bidikara, kuti: “Munyamule, umuponye m’munda wa Naboti Myezereeli.+ Kumbukira kuti iwe ndi ine tinkayenda pambuyo pa Ahabu bambo ake, aliyense atakwera pagaleta lake la mahatchi awiri, pa nthawi imene Yehova anam’temberera+ kuti:
-