Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anawauza kuti: “Izi ndi zimene mfumu yokulamuliraniyo izidzafuna kwa inu:+ Idzatenga ana anu+ kuti azikayenda m’magaleta*+ ake ndi kukwera pamahatchi*+ ake, ndipo ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.+

  • 1 Samueli 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo mfumu inauza asilikali othamanga+ amene anaima pamaso pake kuti: “Tembenukani ndi kupha ansembe a Yehova chifukwa ali kumbali ya Davide. Iwo anali kudziwanso kuti Davide ndi wothawa koma sanaulule kwa ine!”+ Koma atumiki a mfumuwo sanafune kutambasula manja awo kuti akanthe ansembe a Yehova.+

  • 2 Samueli 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Ndiloleni ndithamange ndikapereke uthenga kwa mfumu, chifukwa Yehova wamuweruza kuti amulanditse m’manja mwa adani ake.”+

  • 1 Mafumu 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho Mfumu Rehobowamu inapanga zishango zamkuwa m’malomwake, ndipo inazipereka kwa akulu a asilikali othamanga,+ omwe anali alonda a pakhomo la nyumba ya mfumu, kuti aziziyang’anira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena