Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehoasi mfumu ya Isiraeli anagwira+ Amaziya mfumu ya Yuda, mwana wa Yehoasi, mwana wa Yehoahazi ku Beti-semesiko. Kenako Yehoasi anatenga Amaziya n’kupita naye ku Yerusalemu,+ ndipo anakagumula mpanda wa Yerusalemu kuyambira pa Chipata cha Efuraimu+ mpaka kukafika pa Chipata cha Pakona.+ Anagumula mpata waukulu mikono 400.

  • Nehemiya 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamenepo anthu anatuluka ndi kukatenga zinthu zimenezi ndipo anapangira misasa. Aliyense anapanga msasa pamwamba pa nyumba yake+ komanso m’mabwalo awo, m’mabwalo+ a nyumba ya Mulungu woona, m’bwalo lalikulu+ la Chipata cha Kumadzi+ ndiponso m’bwalo lalikulu la Chipata cha Efuraimu.+

  • Nehemiya 12:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Anadutsanso pamwamba pa Chipata cha Efuraimu,+ Chipata cha Mzinda Wakale,+ Chipata cha Nsomba+ mpaka kukafika pa Nsanja ya Hananeli,+ Nsanja ya Meya+ ndi ku Chipata cha Nkhosa,+ ndipo anaima pa Chipata cha Alonda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena