Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 10:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Chotero iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ n’kuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa la pangano la Yehova+ linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, kuwafunira malo oti amangepo msasa.+

  • 1 Mbiri 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno Davide atangoyamba kukhala m’nyumba yake,+ anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ koma likasa+ la pangano la Yehova likukhala m’chihema chansalu.”+

  • Aheberi 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena