1 Samueli 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+ 1 Samueli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+
10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+
3 Nkhondo inam’kulira kwambiri Sauli, moti pamapeto pake oponya mivi ndi uta anamupeza ndipo anamuvulaza koopsa.+