Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 31:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ngati ndinkalepheretsa chiweruzo cha kapolo wanga wamwamuna,

      Kapena cha kapolo wanga wamkazi pa mlandu ndi ine,

  • Salimo 140:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wolankhula zazikulu* asakhazikike padziko lapansi.+

      Zoipa zisakesake munthu wochita zachiwawa ndipo zimukanthe mobwerezabwereza.+

  • Miyambo 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anzeru ndiwo amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+ koma pakamwa pa wopusa patsala pang’ono kuwonongeka.+

  • Miyambo 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+

  • Miyambo 28:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Munthu wonyada amayambitsa mikangano,+ koma wodalira Yehova adzanenepa.+

  • Miyambo 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kudzikuza kwa munthu wochokera kufumbi kudzamutsitsa,+ koma wa mtima wodzichepetsa adzapeza ulemerero.+

  • Mateyu 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo amamanga akatundu olemera ndi kusenzetsa anthu pamapewa,+ koma eni akewo safuna kusuntha akatunduwo ndi chala chawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena