Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Hamani atalowa, mfumu inam’funsa kuti: “Kodi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu tim’chitire chiyani?”+ Atamva zimenezi, Hamani ananena mumtima mwake kuti: “Kodi winanso ndani amene mfumu ingafune kum’patsa ulemu kuposa ine?”+

  • Miyambo 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+

  • Luka 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+

  • Yakobo 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli.+ N’chifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikweza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena