Miyambo 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+ Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+ Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+
15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+