1 Samueli 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale. 1 Mbiri 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Penueli bambo wa Gedori,+ ndi Ezeri bambo wa Husa. Amenewa ndiwo anali ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata, ndipo Hura anali bambo wa Betelehemu.+ Nehemiya 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amuna a ku Betelehemu+ ndi ku Netofa,+ 188.
12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale.
4 Penueli bambo wa Gedori,+ ndi Ezeri bambo wa Husa. Amenewa ndiwo anali ana a Hura+ mwana woyamba wa Efurata, ndipo Hura anali bambo wa Betelehemu.+