Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 6:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 M’bale wake Asafu+ anali kutumikira mbali ya kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya,+ Berekiya anali mwana wa Simeya,

  • 1 Mbiri 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake.

  • 1 Mbiri 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Davide ndi atsogoleri+ a magulu a anthu otumikira,+ anapatula ena mwa ana a Asafu, a Hemani,+ ndi a Yedutuni,+ kuti azitumikira. Amuna atatuwa anali kulosera ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ ndi zinganga.+ Mwa ana awo anatengamo amuna ena n’kuwaika pa udindo kuti azitumikira.

  • Nehemiya 7:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Oimba,+ ana a Asafu,+ 148.

  • Nehemiya 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mataniya+ mwana wa Mika amene anali mwana wa Zabidi mwana wa Asafu,+ anali wotsogolera nyimbo zotamanda+ Mulungu. Iye anali kutamanda Mulungu pa nthawi ya mapemphero.+ Bakibukiya anali wachiwiri kwa woyang’anira pakati pa abale ake. Panalinso Abada mwana wa Samuwa, Samuwa anali mwana wa Galali, ndipo Galali+ anali mwana wa Yedutuni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena