Levitiko 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli. Numeri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amenewa ndiwo malamulo+ ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa ana a Isiraeli kudzera kwa Mose ku Yeriko, m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+ Salimo 119:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mwatilamula kuti tisunge+Malamulo anu mosamala.+
34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli.
13 Amenewa ndiwo malamulo+ ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa ana a Isiraeli kudzera kwa Mose ku Yeriko, m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+