Deuteronomo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+ Oweruza 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyankha, ana a Isiraeli anauza Yehova kuti: “Tachimwa.+ Inuyo mutichite zilizonse zimene zingakukomereni m’maso mwanu.+ Koma chonde, ingotipulumutsani lero.”+
12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+
15 Poyankha, ana a Isiraeli anauza Yehova kuti: “Tachimwa.+ Inuyo mutichite zilizonse zimene zingakukomereni m’maso mwanu.+ Koma chonde, ingotipulumutsani lero.”+