Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Iye akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,+

      Ndipo manja anga akukunga uta wamkuwa.+

  • Salimo 18:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Mulungu woona ndiye Wobwezera adani anga.+

      Iye amagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuiika kunsi kwa mapazi anga.+

  • Mika 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Otsala a Yakobo adzakhala pakati pa mitundu yambiri ya anthu. Iwo adzakhala ngati mkango pakati pa nyama zakutchire. Adzakhala ngati mkango wamphamvu pakati pa magulu ankhosa, umene umati ukadutsa pakati pa nkhosazo, ndithu umazimbwandira ndi kuzikhadzula+ ndipo sipakhala wozipulumutsa.

  • 2 Atesalonika 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena