Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 143:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+ Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti onse ndi ochimwa+ ndipo ndi operewera pa ulemerero wa Mulungu.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+