27 Mayiyo atafika kwa munthu wa Mulungu woona paphiripo, nthawi yomweyo anam’gwira mapazi.+ Gehazi ataona zimenezo, anabwera pafupi kuti am’kankhe mayiyo.+ Koma munthu wa Mulungu woonayo+ anamuuza kuti: “Musiye,+ mtima wake ukum’pweteka kwambiri.+ Koma Yehova wandibisira,+ sanandiuze.”